Malawian Representatives – Chichewa

 

Malawian flag Stock Photos, Royalty Free Malawian flag Images |  Depositphotos

Mwina timavutika pa nyanja ya nsautso

Mwina timavutika pa nyanja ya nsautso, Ndi namondwe akuopsa amalondola
(Perhaps we suffer on the sea of ​​trouble, And fierce storms follow)
dzuwa, Koma m’dziko langwiro zitachoka
(the sun, But in the perfect world when it is gone)
nkhunguzo,
(the mold,)
Tidzazindikira bwino patsogolo
(We will find out better in advance)

Chorus:
Patsogolo mmene mawa abwera, Pamene oyera adzafika kwawo, Tidzanena nthano tagonjetsa bwanji,
(Before tomorrow comes, When the saints come home, We will tell tales of how we conquered,)
Tidzazindikira bwino patsogolo.
(We will find out better in advance.)

Zofunika zinthuzi nzosoweka m’dzikoli, M’thupi njala ndi usiwa m’munda mulibe m’mela
(These important things are scarce in the world, there is no hunger in the body and no such thing in the field
in malt)

Tikhulupire Mbuye, ndi malinga ndi Mawu,
(Let us believe in the Lord, and according to words,)
Tidzazindikira bwino patsogolo
(We will find out better in advance)

M’mbali zonse zovuta nzosazindikirika, Njira zosiyana zonka ku dziko la lonjezo,
(In all directions the difficulties are unmarked, Different paths to the promised land,)
Mlungu adzatisunga mpaka tsiku la imfa,
(The sun will protect us until the day of death,)
Tidzazindikira bwino patsogolo
(We will find out better in advance)

Ife mwina tigwidwa ndi msampha
(We may be caught in a trap)
wobisika,
(hidden,)
Mtima upweteka tikanena Mawu olakwa;
(The heart hurts when we say wrong words;)
Tikafunsa chifukwa chomwe
(When we ask why)
timayesedwa,
(we are tested,)
Tidzazindikira bwino patsogolo
(We will find out better in advance)